Genesis 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo cholengedwa chilichonse chamoyo cha padziko lapansi, cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, chilichonse chokwawa padziko lapansi, ndi nsomba zonse za m’nyanja, zizikuopani. Tsopano ndapereka zonsezi m’manja mwanu.+
2 Ndipo cholengedwa chilichonse chamoyo cha padziko lapansi, cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, chilichonse chokwawa padziko lapansi, ndi nsomba zonse za m’nyanja, zizikuopani. Tsopano ndapereka zonsezi m’manja mwanu.+