Mateyu 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Pakuti Malemba amati, ‘Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira,+ ndipo uyenera kutumikira+ iye yekha basi.’”+ Mateyu 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Mdyerekezi uja anamusiya,+ ndipo kunabwera angelo ndi kuyamba kum’tumikira.+ Luka 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mdyerekeziyo atamaliza mayesero onsewo, anamusiya kufikira nthawi ina yabwino.+
10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Pakuti Malemba amati, ‘Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira,+ ndipo uyenera kutumikira+ iye yekha basi.’”+