Yesaya 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu okhala m’mizindayo adzafooka manja.+Adzachita mantha kwambiri ndiponso adzachita manyazi.+ Adzakhala ngati zomera zakutchire, ndi udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga+ ndiponso wa m’mizere ya m’munda, ukawauka ndi mphepo yotentha yakum’mawa.+ Yesaya 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Winawake akunena kuti: “Lankhula mofuula!”+ Ndiye wina akuti: “Ndilankhule mofuula za chiyani?” “Anthu onse ali ngati udzu wobiriwira ndipo kukoma mtima kwawo konse kosatha kuli ngati maluwa akutchire.+ 1 Petulo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+
27 Anthu okhala m’mizindayo adzafooka manja.+Adzachita mantha kwambiri ndiponso adzachita manyazi.+ Adzakhala ngati zomera zakutchire, ndi udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga+ ndiponso wa m’mizere ya m’munda, ukawauka ndi mphepo yotentha yakum’mawa.+
6 Tamvera! Winawake akunena kuti: “Lankhula mofuula!”+ Ndiye wina akuti: “Ndilankhule mofuula za chiyani?” “Anthu onse ali ngati udzu wobiriwira ndipo kukoma mtima kwawo konse kosatha kuli ngati maluwa akutchire.+
24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+