Yesaya 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+ Mateyu 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiponso ndikukuuzani kuti, N’chapafupi kuti ngamila ilowe padiso la singano kusiyana n’kuti munthu wolemera alowe mu ufumu wa Mulungu.”+
7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+
24 Ndiponso ndikukuuzani kuti, N’chapafupi kuti ngamila ilowe padiso la singano kusiyana n’kuti munthu wolemera alowe mu ufumu wa Mulungu.”+