Levitiko 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musamalumbire zabodza m’dzina langa+ ndi kuipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova. Mateyu 5:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma ine ndikukuuzani kuti: Usamalumbire+ n’komwe, kutchula kumwamba, chifukwa ndi kumene kuli mpando wachifumu wa Mulungu,+
34 Koma ine ndikukuuzani kuti: Usamalumbire+ n’komwe, kutchula kumwamba, chifukwa ndi kumene kuli mpando wachifumu wa Mulungu,+