Mateyu 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Odala ndi anthu amene akuzunzidwa+ chifukwa cha chilungamo, pakuti ufumu wakumwamba ndi wawo. Yakobo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abale anga, sangalalani pamene mukukumana ndi mayesero osiyanasiyana,+