Mateyu 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mbewu zimene zafesedwa panthaka yabwino, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuzindikira tanthauzo lake, amene amabaladi zipatso. Uyu zipatso 100, uyo 60, winayo 30.”+
23 Mbewu zimene zafesedwa panthaka yabwino, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuzindikira tanthauzo lake, amene amabaladi zipatso. Uyu zipatso 100, uyo 60, winayo 30.”+