Aroma 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu amene sadalira ntchito zake koma amakhulupirira+ Mulungu, amayesedwa wolungama chifukwa cha chikhulupiriro chake,+ pakuti Mulungu amatha kuona munthu wosatsatira malamulo ake kukhala wolungama.
5 Munthu amene sadalira ntchito zake koma amakhulupirira+ Mulungu, amayesedwa wolungama chifukwa cha chikhulupiriro chake,+ pakuti Mulungu amatha kuona munthu wosatsatira malamulo ake kukhala wolungama.