Yohane 8:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndani wa inu amene angandipeze ndi mlandu wa tchimo? Ndipo ngati ndimanena zoona, n’chifukwa chiyani simundikhulupirira?+ Aheberi 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti mkulu wa ansembe amene tili naye si mkulu wa ansembe amene sangatimvere chisoni+ pa zofooka zathu. Koma tili ndi mkulu wa ansembe amene anayesedwa m’zonse ngati ifeyo, ndipo anakhalabe wopanda uchimo.+
46 Ndani wa inu amene angandipeze ndi mlandu wa tchimo? Ndipo ngati ndimanena zoona, n’chifukwa chiyani simundikhulupirira?+
15 Pakuti mkulu wa ansembe amene tili naye si mkulu wa ansembe amene sangatimvere chisoni+ pa zofooka zathu. Koma tili ndi mkulu wa ansembe amene anayesedwa m’zonse ngati ifeyo, ndipo anakhalabe wopanda uchimo.+