Afilipi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu,+ anadzichepetsa ndi kukhala womvera mpaka imfa.+ Anakhala womvera mpaka imfa ya pamtengo wozunzikirapo.*+
8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu,+ anadzichepetsa ndi kukhala womvera mpaka imfa.+ Anakhala womvera mpaka imfa ya pamtengo wozunzikirapo.*+