1 Timoteyo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mofanana ndi zimenezi, ndikufunanso kuti akazi azidzikongoletsa ndi zovala zoyenera, povala mwaulemu+ ndi mwanzeru, osati kudzikongoletsa ndi masitayilo omangira tsitsi, golide, ngale, kapena zovala zamtengo wapatali.+
9 Mofanana ndi zimenezi, ndikufunanso kuti akazi azidzikongoletsa ndi zovala zoyenera, povala mwaulemu+ ndi mwanzeru, osati kudzikongoletsa ndi masitayilo omangira tsitsi, golide, ngale, kapena zovala zamtengo wapatali.+