Genesis 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Udzipangire chingalawa cha mtengo wa mnjale.+ Uchigawe zipindazipinda, ndipo uchimate ndi phula+ mkati ndi kunja komwe.
14 Udzipangire chingalawa cha mtengo wa mnjale.+ Uchigawe zipindazipinda, ndipo uchimate ndi phula+ mkati ndi kunja komwe.