Deuteronomo 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mungaiwale amene anakudyetsani mana+ m’chipululu, chakudya chimene makolo anu sanachidziwe, pofuna kukuphunzitsani kudzichepetsa+ ndi kuti akuyeseni kuti potsirizira pake akuchitireni zabwino.+ Yakobo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 monga mukudziwira kuti chikhulupiriro chanu chikayesedwa, chimabala kupirira.+
16 Mungaiwale amene anakudyetsani mana+ m’chipululu, chakudya chimene makolo anu sanachidziwe, pofuna kukuphunzitsani kudzichepetsa+ ndi kuti akuyeseni kuti potsirizira pake akuchitireni zabwino.+