Yohane 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo,+ mnofu n’ngopanda phindu. Mawu amene ndakuuzaniwa ndiwo mzimu+ ndiponso ndiwo moyo.+
63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo,+ mnofu n’ngopanda phindu. Mawu amene ndakuuzaniwa ndiwo mzimu+ ndiponso ndiwo moyo.+