1 Akorinto 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 moti palibe mphatso+ imene ikuperewera mwa inu, pamene mukudikira mwachidwi kuululidwa+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.
7 moti palibe mphatso+ imene ikuperewera mwa inu, pamene mukudikira mwachidwi kuululidwa+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.