Salimo 90:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti kwa inu zaka 1,000 zili ngati dzulo lapitali,+Ndiponso zili ngati ulonda umodzi wa usiku.*+