Tito 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma abale athu aphunzire kugwira ntchito zabwino kuti athe kupeza zinthu zofunika,+ ndiponso kuti asakhale opanda phindu.+ Chivumbulutso 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, ndakupeza ndi mlandu wakuti wasiya chikondi chimene unali nacho poyamba.+
14 Koma abale athu aphunzire kugwira ntchito zabwino kuti athe kupeza zinthu zofunika,+ ndiponso kuti asakhale opanda phindu.+