Ezekieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atayamba kulankhula nane, mzimu unalowa mwa ine+ ndipo unandiimiritsa kuti ndimvetsere yemwe anali kulankhula ndi ineyo.+ Luka 1:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 monga mmene iye ananenera kudzera pakamwa pa aneneri ake oyera akale,+
2 Atayamba kulankhula nane, mzimu unalowa mwa ine+ ndipo unandiimiritsa kuti ndimvetsere yemwe anali kulankhula ndi ineyo.+