Genesis 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’masiku amenewo ndiponso kupita m’tsogolo, padziko lapansi panali Anefili.* Pa nthawiyo, ana a Mulungu woona anali kugona ndi ana aakazi a anthu ndipo anawaberekera ana. Anawo anali ziphona zakalelo, amuna otchuka.
4 M’masiku amenewo ndiponso kupita m’tsogolo, padziko lapansi panali Anefili.* Pa nthawiyo, ana a Mulungu woona anali kugona ndi ana aakazi a anthu ndipo anawaberekera ana. Anawo anali ziphona zakalelo, amuna otchuka.