Genesis 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene iye anali kuzengereza,+ alendowo, mwa chifundo cha Yehova pa iye,+ anagwira dzanja iyeyo, mkazi wake, ndi ana ake aakazi awiriwo, n’kuwatulutsa kukawasiya kunja kwa mzinda.+
16 Pamene iye anali kuzengereza,+ alendowo, mwa chifundo cha Yehova pa iye,+ anagwira dzanja iyeyo, mkazi wake, ndi ana ake aakazi awiriwo, n’kuwatulutsa kukawasiya kunja kwa mzinda.+