Akolose 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khristuyo, amene ndiye moyo wathu,+ akadzaonetsedwa,+ inunso mudzaonetsedwa limodzi naye mu ulemerero.+ 1 Timoteyo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuti usunge lamulolo. Ulisunge uli wopanda banga ndi wopanda chifukwa chokunenezera, kufikira kuonekera+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.
4 Khristuyo, amene ndiye moyo wathu,+ akadzaonetsedwa,+ inunso mudzaonetsedwa limodzi naye mu ulemerero.+
14 kuti usunge lamulolo. Ulisunge uli wopanda banga ndi wopanda chifukwa chokunenezera, kufikira kuonekera+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.