1 Akorinto 15:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndiponso, monga tilili m’chifaniziro+ cha wopangidwa ndi fumbi uja, tidzakhalanso m’chifaniziro+ cha wakumwambayo. Afilipi 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iyeyo adzakonzanso thupi lathu lonyozekali+ kuti lifanane ndi thupi lake laulemerero.+ Adzatero malinga ndi mphamvu+ imene ali nayo, yotha kugonjetsera+ ngakhale zinthu zonse kwa iye mwini.
49 Ndiponso, monga tilili m’chifaniziro+ cha wopangidwa ndi fumbi uja, tidzakhalanso m’chifaniziro+ cha wakumwambayo.
21 Iyeyo adzakonzanso thupi lathu lonyozekali+ kuti lifanane ndi thupi lake laulemerero.+ Adzatero malinga ndi mphamvu+ imene ali nayo, yotha kugonjetsera+ ngakhale zinthu zonse kwa iye mwini.