1 Yohane 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kusalungama kulikonse ndi tchimo.+ Komabe pali tchimo limene silibweretsa imfa.