Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+ 3 Yohane 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wokondedwa, usamatsanzire zinthu zoipa koma uzitsanzira zabwino.+ Munthu amene amachita zabwino ndi wochokera kwa Mulungu.+ Koma wochita zoipa sadziwa Mulungu.+
15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+
11 Wokondedwa, usamatsanzire zinthu zoipa koma uzitsanzira zabwino.+ Munthu amene amachita zabwino ndi wochokera kwa Mulungu.+ Koma wochita zoipa sadziwa Mulungu.+