Mateyu 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Inu munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti ‘Usaphe munthu.+ Aliyense amene wapha mnzake+ wapalamula mlandu wa kukhoti.’+ Aefeso 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kuwawidwa mtima konse kwa njiru,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata ndiponso mawu achipongwe+ zichotsedwe mwa inu limodzi ndi zoipa zonse.+
21 “Inu munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti ‘Usaphe munthu.+ Aliyense amene wapha mnzake+ wapalamula mlandu wa kukhoti.’+
31 Kuwawidwa mtima konse kwa njiru,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata ndiponso mawu achipongwe+ zichotsedwe mwa inu limodzi ndi zoipa zonse.+