Yohane 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+ Aroma 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anaika miyoyo+ yawo pachiswe chifukwa cha moyo wanga, ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira,+ komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina. 1 Atesalonika 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho popeza timakukondani kwambiri,+ tinali okonzeka kukupatsani uthenga wabwino wa Mulungu. Ndipotu osati uthenga wokha ayi, komanso miyoyo+ yathu yeniyeniyo, chifukwa tinakukondani kwambiri.+
4 Iwo anaika miyoyo+ yawo pachiswe chifukwa cha moyo wanga, ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira,+ komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina.
8 Choncho popeza timakukondani kwambiri,+ tinali okonzeka kukupatsani uthenga wabwino wa Mulungu. Ndipotu osati uthenga wokha ayi, komanso miyoyo+ yathu yeniyeniyo, chifukwa tinakukondani kwambiri.+