Yohane 8:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Wochokera kwa Mulungu amamvetsera mawu a Mulungu.+ Ndiye chifukwa chake inu simumvetsera, chifukwa sindinu ochokera kwa Mulungu.”+ Yohane 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+
47 Wochokera kwa Mulungu amamvetsera mawu a Mulungu.+ Ndiye chifukwa chake inu simumvetsera, chifukwa sindinu ochokera kwa Mulungu.”+
17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+