1 Yohane 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amene amanena kuti: “Ine ndikumudziwa,”+ koma sasunga malamulo ake,+ ameneyo ndi wabodza, ndipo mwa munthu ameneyo mulibe choonadi.+
4 Munthu amene amanena kuti: “Ine ndikumudziwa,”+ koma sasunga malamulo ake,+ ameneyo ndi wabodza, ndipo mwa munthu ameneyo mulibe choonadi.+