Deuteronomo 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse, kuti iwo ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino mpaka kalekale!*+ Deuteronomo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Samala. Uzimvera mawu onsewa amene ndikukuuza,+ kuti zinthu zikuyendere bwino+ mpaka kalekale, iweyo ndi ana ako aamuna obwera m’mbuyo mwako, chifukwa ukatero udzachita chabwino ndi choyenera pamaso pa Yehova Mulungu wako.+
29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse, kuti iwo ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino mpaka kalekale!*+
28 “Samala. Uzimvera mawu onsewa amene ndikukuuza,+ kuti zinthu zikuyendere bwino+ mpaka kalekale, iweyo ndi ana ako aamuna obwera m’mbuyo mwako, chifukwa ukatero udzachita chabwino ndi choyenera pamaso pa Yehova Mulungu wako.+