1 Yohane 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana okondedwa, inu ndinu ochokera kwa Mulungu, ndipo mwagonjetsa anthu amenewo,+ chifukwa amene muli ogwirizana+ naye ndi wamkulu+ kuposa amene ali wogwirizana ndi dziko.+
4 Ana okondedwa, inu ndinu ochokera kwa Mulungu, ndipo mwagonjetsa anthu amenewo,+ chifukwa amene muli ogwirizana+ naye ndi wamkulu+ kuposa amene ali wogwirizana ndi dziko.+