Yohane 5:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso Atate amene anandituma andichitira umboni.+ Inu simunamvepo mawu ake nthawi ina iliyonse, kapena kuona thupi lake.+
37 Komanso Atate amene anandituma andichitira umboni.+ Inu simunamvepo mawu ake nthawi ina iliyonse, kapena kuona thupi lake.+