Yohane 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti monga Atate ali nawo moyo mwa iwo wokha,+ alolanso Mwana kukhala nawo moyo mwa iye yekha.+