Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+ Aroma 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma valani Ambuye Yesu Khristu,+ ndipo musamakonzekere kuchita zilakolako za thupi.+ 1 Petulo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Monga ana omvera, lekani kukhala motsatira+ zilakolako zimene munali nazo kale pamene munali osadziwa.
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+
14 Monga ana omvera, lekani kukhala motsatira+ zilakolako zimene munali nazo kale pamene munali osadziwa.