2 Petulo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa chifukwa chimenechi, nthawi zonse ndizikukumbutsani+ zinthu zimenezi, ngakhale kuti mukuzidziwa kale ndipo ndinu olimba m’choonadi+ chimene munachilandira.+
12 Pa chifukwa chimenechi, nthawi zonse ndizikukumbutsani+ zinthu zimenezi, ngakhale kuti mukuzidziwa kale ndipo ndinu olimba m’choonadi+ chimene munachilandira.+