Luka 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma aliyense wondikana+ ine pamaso pa anthu, adzakanidwa pamaso pa angelo a Mulungu.+