Yohane 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yesu anamuyankha kuti: “Ngati munthu amandikonda, adzasunga+ mawu anga. Atate wanga adzamukonda, ndipo tidzapita kwa iwo ndi kukakhala nawo.+ 2 Yohane 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo chikondi chimenechi chimatanthauza kuti+ tiziyendabe motsatira malamulo ake.+ Monga mmene munamvera kuyambira pachiyambi, lamulo lake ndi lakuti mupitirize kuyenda m’chikondi,+
23 Yesu anamuyankha kuti: “Ngati munthu amandikonda, adzasunga+ mawu anga. Atate wanga adzamukonda, ndipo tidzapita kwa iwo ndi kukakhala nawo.+
6 Ndipo chikondi chimenechi chimatanthauza kuti+ tiziyendabe motsatira malamulo ake.+ Monga mmene munamvera kuyambira pachiyambi, lamulo lake ndi lakuti mupitirize kuyenda m’chikondi,+