Ezekieli 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo adzakhala muhema wanga.+ Ine ndidzakhaladi Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.+