Yesaya 54:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nsanja za pamakoma ako ndidzazimanga ndi miyala ya rube, ndipo zipata zako ndidzazimanga ndi miyala yofiira ngati moto.+ Zizindikiro za m’malire ako onse ndidzazimanga ndi miyala yamtengo wapatali.
12 Nsanja za pamakoma ako ndidzazimanga ndi miyala ya rube, ndipo zipata zako ndidzazimanga ndi miyala yofiira ngati moto.+ Zizindikiro za m’malire ako onse ndidzazimanga ndi miyala yamtengo wapatali.