Afilipi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, mulimonse mmene tapitira patsogolo, tiyeni tipitirize kupita patsogolo mwa kuyenda moyenera+ m’njira yomweyo.
16 Komabe, mulimonse mmene tapitira patsogolo, tiyeni tipitirize kupita patsogolo mwa kuyenda moyenera+ m’njira yomweyo.