Aefeso 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 N’chifukwa chake iye akunena kuti: “Dzuka,+ wogona iwe! Uka kwa akufa,+ ndipo Khristu adzakuunika.”+
14 N’chifukwa chake iye akunena kuti: “Dzuka,+ wogona iwe! Uka kwa akufa,+ ndipo Khristu adzakuunika.”+