Mateyu 24:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero khalanibe maso chifukwa simukudziwa tsiku limene Ambuye wanu adzabwere.+ Luka 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma dziwani kuti mwininyumba atadziwa nthawi yobwera mbala, angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.+
39 Koma dziwani kuti mwininyumba atadziwa nthawi yobwera mbala, angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.+