Hoseya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+ 1 Akorinto 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi anthu inu mwakhuta kale eti? Mwalemera kale, si choncho?+ Kodi mwayamba kale kulamulira monga mafumu+ popanda ife? Ndikanakondadi mukanayamba kulamulira monga mafumu, kuti ifenso tilamulire limodzi nanu monga mafumu.+
8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+
8 Kodi anthu inu mwakhuta kale eti? Mwalemera kale, si choncho?+ Kodi mwayamba kale kulamulira monga mafumu+ popanda ife? Ndikanakondadi mukanayamba kulamulira monga mafumu, kuti ifenso tilamulire limodzi nanu monga mafumu.+