Genesis 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiika utawaleza+ mumtambo, kuti ukhale chizindikiro cha pangano pakati pa ine ndi dziko lapansi.