Chivumbulutso 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atamatula chidindo chachinayi, ndinamva mawu a chamoyo chachinayi+ chikunena kuti: “Bwera!”