Chivumbulutso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinaona Mwanawankhosa+ atamatula chidindo chimodzi mwa zidindo 7 zija,+ ndipo ndinamva chamoyo chimodzi mwa zamoyo zinayi zija+ chikulankhula ndi mawu ngati kugunda kwa bingu kuti: “Bwera!”+
6 Ndinaona Mwanawankhosa+ atamatula chidindo chimodzi mwa zidindo 7 zija,+ ndipo ndinamva chamoyo chimodzi mwa zamoyo zinayi zija+ chikulankhula ndi mawu ngati kugunda kwa bingu kuti: “Bwera!”+