Chivumbulutso 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsoka limodzilo linapita. Koma masoka ena awiri+ anali kubwera pambuyo pa zimenezi. Chivumbulutso 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsoka+ lachiwiri linapita. Koma tsoka lachitatu linali kubwera mofulumira.