Chivumbulutso 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako ndinaona angelo 7+ ataimirira pamaso pa Mulungu, ndipo anapatsidwa malipenga 7.