Yobu 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika? Chivumbulutso 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+
21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika?
16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+