1 Akorinto 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 koma ngati mkazi ali ndi tsitsi lalitali, ndi ulemerero kwa iye?+ Zili choncho chifukwa wapatsidwa tsitsi lakelo m’malo mwa chovala kumutu.+ Aefeso 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipotu, monga mmene mpingo umagonjerera Khristu, akazinso agonjere amuna awo m’chilichonse.+
15 koma ngati mkazi ali ndi tsitsi lalitali, ndi ulemerero kwa iye?+ Zili choncho chifukwa wapatsidwa tsitsi lakelo m’malo mwa chovala kumutu.+