Chivumbulutso 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzombelo silinaloledwe kupha anthuwo, koma linauzidwa kuti liwazunze+ miyezi isanu. Ndipo kuzunzika kwawo kunali kofanana ndi mmene munthu amazunzikira akalumidwa ndi chinkhanira.+
5 Dzombelo silinaloledwe kupha anthuwo, koma linauzidwa kuti liwazunze+ miyezi isanu. Ndipo kuzunzika kwawo kunali kofanana ndi mmene munthu amazunzikira akalumidwa ndi chinkhanira.+